Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 8:63 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Solomo anaphera nsembe yamtendere, yophera kwa Yehova ng'ombe zikwi makumi awiri mphambu ziwiri, ndi nkhosa zikwi zana limodzi mphambu makumi awiri. Momwemo mfumu ndi ana a Israyeli onse anapereka nyumbayo ya Yehova.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 8

Onani 1 Mafumu 8:63 nkhani