Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 8:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ansembe analonga likasa la cipangano ca Yehova kumalo kwace, ku monenera mwa nyumba, ku malo opatulikitsa, munsi mwa mapiko a akerubi,

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 8

Onani 1 Mafumu 8:6 nkhani