Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 8:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anatenga likasa la Yehova, ndi cihema cokomanako, ndi zipangizo zonse zopatulika, zinali m'cihemamo, inde zimenezi anazitenga ansembe ndi Alevi.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 8

Onani 1 Mafumu 8:4 nkhani