Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 8:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Kuyambira tsiku lakuturutsa Ine anthu anga Aisrayeli m'dziko la Aigupto, sindinasankha mudzi uli wonse mwa mafuko onse a Israyeli kumangamo nyumba yokhalamo dzina langa, koma ndinasankha Davide kukhala mfumu ya anthu anga Aisrayeli.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 8

Onani 1 Mafumu 8:16 nkhani