Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 8:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nati iye, Wolemekezeka ndi Yehova Mulungu wa Israyeli amene analankhula m'kamwa mwace ndi Davide atate wanga, nakwaniritsa ndi dzanja lace, nati,

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 8

Onani 1 Mafumu 8:15 nkhani