Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 7:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Popeza iyeyu anaunda nsanamira ziwiri zamkuwa, msinkhu wace wa imodzi unali mikono khumi mphambu isanu ndi itatu; ndipo cingwe ca mikono khumi mphambu iwiri cinayesa thupi la nsanamira imodzi.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 7

Onani 1 Mafumu 7:15 nkhani