Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 7:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Iyeyo anali mwana wace wa mkazi wamasiye wa pfuko la Nafitali, atate wace anali munthu wa ku Turo, mfundi wa mkuwa; ndipo iye anadzala ndi nzeru ndi luntha ndi luso kugwira nchito zonse za mkuwa. Ndipo anadza kwa mfumu Solomo namgwirira nchito zace zonse.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 7

Onani 1 Mafumu 7:14 nkhani