Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 20:31 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo anyamata ace anati kwa iye, Taonani, tidamva ife kuti mafumu a nyumba ya Israyeli ndi mafumu acifundo; tiyeni tibvale ciguduli m'cuuno mwathu, ndi zingwe pamitu pathu, titurukire kwa mfumu ya Israyeli, kapena adzakusungirani moyo.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 20

Onani 1 Mafumu 20:31 nkhani