Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 20:32 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Motero anabvala ciguduli m'cuuno mwao, ndi zingwe pamitu pao, nafika kwa mfumu ya Israyeli, nati, Kapolo wanu Benihadadi ati, Ndiloleni ndikhale ndi moyo. Nati iye, Akali moyo kodi? Ndiye mbale wanga.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 20

Onani 1 Mafumu 20:32 nkhani