Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 18:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

pakuti pamene Yezebeli anapulula aneneri a Yehova, Obadiya anatenga aneneri zana limodzi, nawabisa makumi asanu asanu m'phanga, nawadyetsa mkate ndi madzi.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 18

Onani 1 Mafumu 18:4 nkhani