Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 17:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nati iye, Pali Yehova Mulungu wako, ndiribe mkate, koma kaufa dzanja limodzi kali m'mbiya, ndi mafuta pang'ono m'nsupa; ndipo taona, ndirikutola nkhuni ziwiri kuti ndikadziphikire odekha ndi mwana wanga, tidye, tife.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 17

Onani 1 Mafumu 17:12 nkhani