Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 17:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo m'mene analikumuka kukatenga iye anamuitananso, nati, Unditengerenso kanthongo ka mkate m'dzanja lako.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 17

Onani 1 Mafumu 17:11 nkhani