Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 17:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Tsono iye ananyamuka namka ku Zarefati, nafika ku cipata ca mudzi; ndipo taona mkazi wamasiye anali kutola nkhuni; ndipo iye anamuitana, nati, Unditengere madzi pang'ono m'cikho, ndimwe.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 17

Onani 1 Mafumu 17:10 nkhani