Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 15:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo mfumu Asa anamemeza Ayuda onse, osatsala ndi mmodzi yense; natuta miyala ya ku Rama, ndi mitengo yomwe, akamange nayo Basa; ndi mfumu Asa anamangira Geba wa ku Benjamini, ndi Mizipa.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 15

Onani 1 Mafumu 15:22 nkhani