Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 11:37 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndidzakutenga iwe, ndipo udzacita ufumu monga umo ukhumbira moyo wako, nudzakhala mfumu ya Israyeli.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 11

Onani 1 Mafumu 11:37 nkhani