Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 11:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mbale wa Takipenesi anamuonera Genubati mwana wace, ameneyo Takipenesi anamletsera kuyamwa m'nyumba ya Farao, ndipo Genubati anakhala m'banja la Farao pamodzi ndi ana amuna a Farao.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 11

Onani 1 Mafumu 11:20 nkhani