Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 11:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Farao anamkomera mtima ndithu Hadadiyo, nampatsa mkazi ndiye mbale wa mkazi wace, mbale wace wa Takipenesi mkazi wamkulu wa mfumu.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 11

Onani 1 Mafumu 11:19 nkhani