Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 10:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mfumu Solomo ananinkha mfumu yaikazi ya ku Seba cifuniro cace conse anacipempha iye, osawerenga cimene Solomo anamninkha mwa ufulu waceo Momwemo iye anabwerera namukanso ku dziko lace, iyeyo ndi anyamata ace.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 10

Onani 1 Mafumu 10:13 nkhani