Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 10:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mfumu inasema mitengo yambawayo, ikhale mizati ya nyumba ya Yehova, ndi ya nyumba ya mfumu; ndiponso azeze ndi zisakasa za oyimbawo; siinafika kapena kuonekanso mpaka lero mitengo yotero yambawa.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 10

Onani 1 Mafumu 10:12 nkhani