Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 1:53 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Tsono mfumu Solomo anatuma anthu nakamtsitsa ku guwa la nsembe. Iye nadza, nagwadira mfumu Solomo; Solomo nati kwa iye, Pita kwanu.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 1

Onani 1 Mafumu 1:53 nkhani