Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 1:52 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Solomo anati, iye akakhala munthu woyenera silidzagwa pansi tsitsi lace limodzi lonse; koma mukapezeka mwa iye coipa, adzafadi.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 1

Onani 1 Mafumu 1:52 nkhani