Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 1:52-53 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

52. Ndipo Solomo anati, iye akakhala munthu woyenera silidzagwa pansi tsitsi lace limodzi lonse; koma mukapezeka mwa iye coipa, adzafadi.

53. Tsono mfumu Solomo anatuma anthu nakamtsitsa ku guwa la nsembe. Iye nadza, nagwadira mfumu Solomo; Solomo nati kwa iye, Pita kwanu.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 1