Ndipo kudzacitika kuti ali yense wa mabanja a dziko wosakwera kumka ku Yerusalemu kulambira mfumu Yehova wa makamu, pa iwowa sipadzakhala mvula.