Kulandira kwao kunacitika ndi kulota maere, monga Yehova adalamulira mwa dzanja la Mose, kunena za mapfuko asanu ndi anai ndi pfuko logawika pakati.