Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yoswa 14:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo awa ndi maiko ana a Israyeli anawalanda m'dziko la Kanani, amene Eleazare wansembe, ndi Yoswa mwana wa Nuni, ndi akulu a nyumba za atate a mapfuko a ana a Israyeli, anawagawira.

Werengani mutu wathunthu Yoswa 14

Onani Yoswa 14:1 nkhani