Pakuti Yehova watero kwa ine, Ine ndidzakhala cete, ndipo ndidzayang'ana mokhala cete, ndipo ndidzayang'ana mokhalamo Ine, monga kuwala kotentha kwa dzuwa, monga mtambo wa mame m'kutentha kwa masika.