Komatu amkhaliraupo kuti amkankhire pansi ulemu wace;Akondwera nao mabodza;Adalitsa ndi m'kamwa mwao, Koma atemberera mumtima.