Indedi, ndinalinganiza ndi kutontholetsa moyo wanga;Ngati mwana womletsa kuyamwa amace,Moyo wanga ndiri nao ngati mwana womletsa kuyamwa.