Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yohane 7:23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ngati munthu alandira mdulidwe tsiku la Sabata, kuti cilamulo ca Mose cingapasulidwe; kodi mundikwiyira Ine, cifukwa ndamciritsadi munthu tsiku la Sabata?

Werengani mutu wathunthu Yohane 7

Onani Yohane 7:23 nkhani