Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yohane 7:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kunali kung'ung'udza kwambiri za iye m'makamu a anthu; ena ananena, kuti, Ali wabwino; koma ena ananena, lai, koma asoceretsa khamu la anthuwo.

Werengani mutu wathunthu Yohane 7

Onani Yohane 7:12 nkhani