Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yohane 21:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Simoni Petro ananena nao, ndinka kukasodza. Ananena naye, Ifenso tipita nawe. Anaturuka, nalowa m'ngalawa; ndipo m'usiku muja sanagwira kanthu.

Werengani mutu wathunthu Yohane 21

Onani Yohane 21:3 nkhani