Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yohane 21:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Yesu ananena nao, Idzani mufisule. Koma palibe mmodzi wa akuphunzira anatha kumfunsa iye, Ndinu yani? podziwa kuti ndiye Ambuye.

Werengani mutu wathunthu Yohane 21

Onani Yohane 21:12 nkhani