Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yohane 21:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa cace Simoni Petro anakwera m'ngalawa nakokera khoka kumtunda Iodzala ndi nsomba zazikuru, zana limodzi, ndi makumiasanu ndi zitatu; ndipo zingakhale zinacuruka kotere, kokha silinang'ambika.

Werengani mutu wathunthu Yohane 21

Onani Yohane 21:11 nkhani