Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yohane 21:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Zitapita izi Yesu anadzionetseranso kwa akuphunzira ace ku nyanja ya Tiberiya. Koma anadzionetsera cotere.

2. Anali pamodzi Simoni Petro, ndi Tomasi, wochedwa Didimo, ndi Natanayeli wa ku Kana wa ku Galileya, ndi ana a Zebedayo, ndi awiri ena a akuphunzira ace.

Werengani mutu wathunthu Yohane 21