Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yohane 18:37 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo Pilato anati kwa iye, Nanga kodi ndiwe Mfumu? Yesu anayankha, Munena kuti ndine Mfumu. Ndinabadwira ici Ine, ndipo ndinadzera ici kudza ku dziko lapansi, kuti ndikacite umboni ndi coonadi. Yense wakukhala mwa coonadi amva mau anga.

Werengani mutu wathunthu Yohane 18

Onani Yohane 18:37 nkhani