Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yohane 10:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Wolipidwa amene sakhala mbusa, amene nkhosa siziri zace za yekha, aona mmbulu ulinkudza, nasiya nkhosazo, nathawa; ndipo mmbulu uzikwatula, nuzibalalitsa;

Werengani mutu wathunthu Yohane 10

Onani Yohane 10:12 nkhani