Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Tito 1:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Zonse ziyera kwa iwo amene ayera mtima; koma kwa iwo odetsedwa ndi osakhulupira kulibe kanthu koyera; komatu zadetsedwa nzeru zao ndi cikumbu mtima cao.

Werengani mutu wathunthu Tito 1

Onani Tito 1:15 nkhani