Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Mateyu 21:32 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Popeza Yohane anadza kwa inu m'njira ya cilungamo, ndipo simunamveraiye; koma amisonkho ndi akazi aciwerewere anammvera iye; ndipo inu, m'mene munaciona, simunalapa pambuyo pace, kuti mumvere iye.

Werengani mutu wathunthu Mateyu 21

Onani Mateyu 21:32 nkhani