Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Marko 9:47 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ngati diso lako likulakwitsa ulikolowole; kulowa iwe m'Ufumu wa Mulungu ndi diso limodzi kuli kwabwino koposa ndi kukhala ndi maso awiri ndi kuponyedwa m'gehena;

Werengani mutu wathunthu Marko 9

Onani Marko 9:47 nkhani