Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Marko 12:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Iye anayamba kulankhula nao m'mafanizo. Munthu analima munda wamphesa, nauzunguniza ndi linga, nakumba moponderamo mphesa, namanga nsanja, naukongoletsa kwa olima munda, namuka kwina.

Werengani mutu wathunthu Marko 12

Onani Marko 12:1 nkhani