Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Macitidwe 9:39 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Petro anayamuka, napita nao. M'mene anafikako, anapita naye ku cipinda ca pamwamba; ndipo amasiye onse anaimirirapo pali iye, nalira, namuonetsa maraya ndizobvala zimene Dorika adasoka, pamene anali nao pamodzi.

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 9

Onani Macitidwe 9:39 nkhani