Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Macitidwe 9:38 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo popeza Luda ndi pafupi pa Yopa, m'mene anamva ophunzirawo kuti Petro anali pomwepo, anamtumizira anthu awiri, namdandaulira, Musacedwa mudze kwa ife.

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 9

Onani Macitidwe 9:38 nkhani