Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Macitidwe 9:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anacoka Hananiya, nalowa m'nyumbayo; ndipo anaika manja ace pa iye, nati, Saulo, mbale, Ambuye wandituma ine, ndiye Yesu amene anakuonekerani pa njira wadzerayo, kuti upenyenso, ndi kudzazidwa ndi Mzimu Woyera.

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 9

Onani Macitidwe 9:17 nkhani