Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Macitidwe 8:2-4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

2. Ndipo anamuika Stefano anthu opembedza, namlira maliro akuru.

3. Ndipo Saulo anapasula Mpingo, nalowa m'nyumba m'nyumba, nakokamo amuna ndi akazi, nawaika m'ndende.

4. Pamenepo ndipo iwo akubalalitsidwa anapitapita nalalikira mauwo.

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 8