Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Macitidwe 8:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Saulo analikubvomerezana nao pa imfa yace. Ndipo tsikulo kunayamba kuzunza kwakukuru pa Mpingo unali m'Yerusalemu; ndipo anabalalitsidwa onse m'maiko a Yudeya ndi samariya, koma osati atumwi ai.

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 8

Onani Macitidwe 8:1 nkhani