Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Macitidwe 6:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma masiku awo, pakucurukitsa ophunzira, kunauka cidandaulo, Aheleniste kudandaula pa Ahebri, popeza amasiye ao anaiwalika pa citumikiro ca tsiku ndi tsiku.

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 6

Onani Macitidwe 6:1 nkhani