Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Macitidwe 4:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo m'mene adamva, anakweza mau kwa Mulungu ndi mtima umodzi, nati, Mfumu, Inu ndinu wolenga thambo la kumwamba ndi dziko, ndi nyanja, ndi zonse ziri m'menemo;

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 4

Onani Macitidwe 4:24 nkhani