Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Macitidwe 24:1-3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Ndipo atapita masiku asanu anatsika mkulu wa ansembe Hananiya pamodzi ndi akuru ena, ndi wogwira moyo dzina lace Tertulo; ndipo anafotokozera kazembeyo za kunenera Paulo.

2. Ndipo pamene adamuitana, Tertulo anayamba kumnenera ndi kunena.Popeza tiri nao mtendere wambiri mwa inu, ndipo mwa kuganiziratu kwanu muukonzera mtundu wathu zotiipsa,

3. tizilandira ndi ciyamiko conse, monsemo ndi ponsepo, Felike womveka inu.

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 24