Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Macitidwe 24:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo atapita masiku asanu anatsika mkulu wa ansembe Hananiya pamodzi ndi akuru ena, ndi wogwira moyo dzina lace Tertulo; ndipo anafotokozera kazembeyo za kunenera Paulo.

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 24

Onani Macitidwe 24:1 nkhani