Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Macitidwe 23:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Ndipo Paulo, popenyetsetsa a m'bwalo la akuru anati, Amuna, abale, ndakhala ine pamaso pa Mulungu ndi cikumbu mtima cokoma conse kufikira lero lomwe.

2. Ndipo mkulu wa ansembe Hananiya analamulira akuimirirako ampande pakamwa pace.

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 23